Appreciation to Lilongwe City Council

17-Mar-2017 | 12:20

Let me commend Lilongwe City Council for stepping up efforts to keep the city clean.

Nkhani ya ukhondo ku Kawale 1

17-Mar-2017 | 15:23

Ndati ndipempheko atsogoleri athu kuti akambirane ndi akuluakulu apa Kawale health centre kuti pakhale njira yowonetsetsa kuti anthu sakutaya zinyala paseli pa chipatalachi. Kuunjikana kwa zinyalala pamalopa kukuika miyoyo ya ana athu pachiophyezo chifukwa ena amapita kukasewerapo

Pempho la Bin pa msika wa Mbayani

17-Mar-2017 | 15:26

Tati tipempheko kudzera mwa Khansala wathu kuno ku Mbayani kuti tikufuna Bin yaikulu yotayamo zinyala chifukwa anthu akumataya zinyalala ku njanji ndipo izi zikubweretsa mphepo yoyipa kwa anthu okhala nyumba zakufupi ndi kumalowa.

Pa Msika Wa Mboni Kwa Mtsiliza Palibe Zimbudzi

28-Mar-2017 | 05:21

Kuno kwa Mtsiliza pa msika wathu wa Mboni palibe zimbudzi.

Leakage in Sewer System *RESOLVED*

27-Apr-2017 | 14:48

There seems to be a leakage in the sewer system from the college of health sciences Blantyre campus as can be observed in the attached picture. This has resulted in waste spilling out to the narrow path that stems out of the high-way at Ginnery corner leading to chitawira. May the relevant authorities at Blantyre city council please engage management at the college.

Tikupempha nawo ma skipper kuno ku Makata

08-Jun-2017 | 10:54

Kuno ku Ndirande Makata tili ndi pempho ku Khonsolo kuti atibweretsere ma skipper mmaka pa nsika waukulu. Ukhondo palibe. Ine Naomi Sunduza

Sanitation Concern in Mzuzu city

06-Jul-2017 | 16:29

I would like to humbly request the authorities at Mzuzu city council to do something with regards policing provision of possible pay toilets or anything that make people to stop urinitating everywhere in some parts of the city like between Banja la mtsogolo and the mosque, and from Taifa market through Usiska Resthouse.

Pempho loti adzochose zinyalala *Resolved*

10-Jul-2017 | 13:33

Chi Bin cha pa msika wa pa Kachere chadzadza, chonde abwere kudzachotsa

Atiganizire nkhani ya ukhondo ku Makhetha

12-Jul-2017 | 01:34

Kuno ku Makhetha pa clinic zimbuzi sizili bwino, ngati kuli kotheka atsogoleri athu kapena amabungwe achitepo kanthu

Sewer Leakage Area 18A *Resolved*

18-Jul-2017 | 13:28

The sewer line passing through Area 18A is leaking and there is a mix up with Lilongwe Water Board pipes. I just took note of the quality of water coming out of the taps.

Kwa Dekezga ma Latrine kulibe

20-Jul-2017 | 12:29

Kuno kwa Dekezga Masasa ward tikufuna ma latrine ngati amene ali kwa Geza mugomo

Pempho la pa Msika wa Target

20-Jul-2017 | 11:50

Kuno ku Mchengautuba East pa msika wa Target palibe nkhando, chonde atithandize