There is a sewege brokage in Soche East
Kusatuluka kwa madzi mmalo ena oyandikira pa town assembly kuno ku Kasungu kukweza chiophyeza chakufala kwa matenda odza Kamba ka Ntchetche
Ngalande za mu msika ndi zosafukula kuno ku Kasungu chinthu chomwe chikupangisa kuti madzi azilowa pamalo ogulitsira malonda
Kuno ku Kasungu misika yambiri ing'onoing'ono mulibe ma toilet koma ma tiketi timaduladaily. Kodi ndalamazo zimagwira ntchito yanji
Ndati ndipemphe nawo chithandizo choti khonsolo itibweresere bin yayikulu pa msika wa Apostolic. Malowa akubweresa chiophyezo cha matenda chifukwa anthu zinyalala akungotaya mosasamala
Ngalande za pa msika waukulu wa Kasungu ndi zosafukula zomwe zikuchititsa kuti madzi adzilowa mu msika chonde atithandize