Waste Collection

23-Aug-2016 | 09:52

Zinandisangalatsa kuwona a city akudzatenga zinyalala mudela lathu izi ndi zithu zabwino ndipo mupitilize a city koma pa msika wa old gualiver pali zinyalala ndipo sipawoneka bwino komaso pamanunkha chonde mudzatiwoneleko kuno ku gualiver, area 49.

Pempho Kwa Anzanga Kuno Kwa Senti

21-Aug-2016 | 13:39

Kuno kwa Centi zinyalala timangotaya paliponse, penpho langa nali, tiyesese pa tokha ngati anthu amudera kutaya zinyalala mosamala

Yankho pa kusaoledwa kwa Zinyalala pa Nsika wa Mtandile

29-Aug-2016 | 19:59

Chigalimoto sichifikadi kuzaola zinyalala chifukwa nsika wa Mtandire amapanga collection ya ma market fees okha.Pano pali kukambirana kuti City Council izitolela yokha ma fees pambuyo pake chigalimoto chizibwera. A Soko. Cllr Mtandile Ward

Sanitation Lilongwe City

03-Sep-2016 | 10:32

Kudos to Lilongwe City Council for stepping up efforts to keep the city clean

Need for action *Resolved*

14-Sep-2016 | 17:07

Along Paul kagame road on the turn to Shire building there is a sory sight of waste. is it a problem of improper dumping of waste or non collection of refuse

Umve pa Mzuzu Health Centre *Resolved*

23-Jul-2016 | 19:11

Umve pa mzuzu health centre kod antchito akugwira ntchito yanji makamaka ku ma toilet kukuwonjeza umve wake ndalama za boma zikupita kut?

Appreciation Waste Collection Zingwangwa

12-Sep-2016 | 06:33

Thank you to those responsible for clearing waste that had been accumulating at Zingwangwa market.

Vuto la zinyalala pa mlatho wa pazambiya

22-Oct-2016 | 11:01

Pali vuto kuno kundilande'pa brige yapazambiya padzadza zinyalara-chonde tinthandinzeni.

ZINYALALA NDIRANDE MAKATA MARKET *Resolved*

23-Oct-2016 | 10:35

kuno ku msika wa ndirande zinyalala ziri pali ponse.Akhonsolo achitepo kanthu.

Sanitation concern *Resolved*

03-Nov-2016 | 16:40

Would our Councilor for Chilinde 2 please take up the issue of sanitation with Chibuku officilas because their people working at Chikwaye tarven are just dumping waste anyhow

Chilinde 1 tikufuna ma toilet pa msika

04-Nov-2016 | 13:02

Kuno ku Chilinde 1 pempho lathu ndi lakuti amange ma toilet pa msika. inde zinyalala amazachotsa komabe tiketi yomwe timadula athaso kutikonzera ma toilet akhonsolo

Non removal of waste Kawale 1

03-Nov-2016 | 15:07

Here in Kawale 1 our request is that our councilor should engage the city council so that the waste removal service should also be collecting waste accumulating at the Health centre