City Council please come and empty waste dustbin *RESOLVED*

04-Nov-2016 | 15:16

I humbly request the Lilongwe city council to please come and empty the waste dustbin at Mchesi market. Waste is overflowing

Tiyamikire Khansala Mike Chimzukira

06-Nov-2016 | 07:52

Ndati ndiyamikire Khansala wa Mbidzi ward Mike Chimzukira chifukwa choika ma bin mu malo ambiri ku old town kuti ukhondo upite patsogolo. anthu nafe pa ife tokha titengepo gawo. Zelesi Kathumba wa zikwama

Tithokoze kuno ku Chilomoni ward

02-Nov-2016 | 08:02

Kuno ku Chilomoni ward titi zikomo adazachotsa zinyala pa beehive

Response to sanitation concern

03-Nov-2016 | 16:51

Thanks for your notification (about engaging Chibuku on sanitation) but i have already engaged them to do as said. Once again thank u keep on updating me. Gibson Nyirenda - Councillor Chilinde II

Ukhondo suli bwino kuno kwa Tsabango

03-Nov-2016 | 18:23

kuno Ku area23 tsabango 1 kuli vuto lakut pamanda agologota mbalimbali mwamanda akumatayamo zinyalala nde awonepo

Appreciation to Lilongwe City Council

07-Nov-2016 | 06:38

We would like to appreciate the pro activeness of Lilongwe city council in waste collection and sanitation. As you can see in the picture, members of a clean up Lilongwe task force clearing up waste in Mwenyekondo

Ukhondo sulibwino ku Masasa

19-Nov-2016 | 14:59

kuno ku masasa ma barber man yotaya sisi bweka am vincent doesmatter

Tichenjere nyengo ya mvula kuno ku Nsanje

27-Nov-2016 | 15:55

kuno ku Nsanje mvula yayambapo ndye ndi mango zati mbwee zofunika azaumoyo achite watchout

Ukhondo kulibe kuno ku Dwangwa

27-Nov-2016 | 13:56

Kuno ku Dwangwa ukasi area za mumtoilet zimacita kuyenda ngati mtsinje m'manyumba mwathu. akhonsolo achitepo kanthu

Atiganizire azaumoyo kuno ku Chiwembe

18-Dec-2016 | 15:49

Kuchokera ku Chiwembe tikudandaula, Pipe ya sewage inathoka kalekale moti nyasi zikukolezera matendakwa anthu kuno ndinso opanga biziness mu nsika wa limbe

Health threat in Area 36

14-Dec-2016 | 16:23

Am Moses from Area 36, mine is a concern that at Phwetekere market where they sell chicken parts there is great lack of hygiene, whose role is it to supervise and or take action on this. Actually at times these people even sell nkhuku zowola. What is the responsibility of the City Council on this?

Waste Accumulation in Falls Estate

27-Dec-2016 | 08:40

As it can be observed in the attached picture, waste has accumulated dangerously in Falls close to Msonkhamanja CCAP. This is because over the past two weeks the City Council did not come through to empty the waste storage dustbin at the dumping site. This is not only an eye sore but also a health threat. Action should be taken and fast.