Yankho pa pempho la mseu ku Zolozolo

20-Nov-2016 | 13:48

mukunena miseu yonse kapena umodzi? ndipo para niumodzi uli mwa blockleader njani? Stafford Khunga - Khansala

Atithandize kuno ku chiputula

21-Nov-2016 | 08:52

Ndikupempha ngati kuli kotheka pa mjirijiri butchery tikamapita pa 4ways ya king shaka bar bridge linabooka komanso tikamapita ku ching'ambo from up chiputula primary pafupi ndi seventhday church. andrew chavula concerned citizen

Atikonzere nseu kuno ku ZoloZolo

20-Nov-2016 | 04:45

Tati tipemphe nawo kuti Khansala wathu kuno ku Zolozolo east atikonzere nseu wa kwa BagiDadi

Pempho kuno ku Makata

03-Dec-2016 | 17:50

Kuno kwa T/A Makata ku Blantyre, bridge ya pa mtsinje wa Mlombozi inakokoloka chaka chatha,koma mpakana pano sunakonzedwe. Tiyembekezere kuti ukonzedwa liti,chifukwa nyengo yamvula ndiye yafikanso

Pempho kuno kwa Jokala

09-Dec-2016 | 08:22

Tati tipemphe nawo kudzera pa Mzinda kuti atithandize kuno kwa Jokala ku Zomba, nkhani ya mseu, mseu wathu kuno sulibwino. Matias Kalemba

Pempho kuno ku Area 36 atikonzere bridge

16-Dec-2016 | 16:08

Chonde brige yolumikiza area 36 ndi tumbwe,payelea ndi kupita kwamitengo,akufuna padzafe kaye munthu? nafenso anthu khalidwe loba mitengo silabwino. Hardson Lefan.champhepete village (area 36,LL).

Pempho kuno kwa Naphiyo

19-Dec-2016 | 16:44

Ine ndim'nyamata ochokela ku chiladzulu south,koma khawa zanga zili pa khansala wanthu naphiyo,pali mulatho wachimwawa umene walumikiza mafumu awili,asakwata komaso mangulama mulatho wapakati pamafumu awili amenewa sulibwino konse,moti sindikudziwa ngati phungu wadela limeneli amene ali josefe mwanamvekha akudziwa zamavuto amenewa,mwachidule inu a Mzinda tapitani kuchiladzulu south kwa t/a nkalo mudzi mwamatope,siliya,ngoniwa,misomali,sakwata,mangulama,mwamidzi yochepa chabe muone mabvuto,ndimakuvetsesani ndim'mene mumapangila kapena kufufuzila zinthu, ine dzinalanga ndi evans mpethela namuku

Vuto la mseu ku Zolozolo East

07-Jan-2017 | 05:04

Suzgo kuno ku Zolozolo ni mseu

Request to upgrade road

10-Jan-2017 | 13:39

In Zolozolo West; the road from CCAP through Bagidadi area needs upgrading. We engaged our councilor before and we were told that it is amongst the roads for consideration under the MASAF project but we don’t know when.

Mavuto omwe tili nawo kuno ku Namiyango

26-Jan-2017 | 17:01

Kuno ku mamiyango vuto ndi madzi ndi magetsi komanso miseu silibwino

Tikupempha nawo nseu watala kuno ku Namiyango

26-Jan-2017 | 00:04

Kuno kunamiyango tikupempha nawo nseu watala ngati anzathu ku Mthandizi

Atikonzere mseu kuno ku Chiputula

25-Jan-2017 | 17:01

Kuno ku Chiputula ku Mzuzu mseu suli bwino. Tipemphe nawo khansala wathu kuti atithandize