Kuthokoza Atikonzera Nseu kwa Chilinde

19-Aug-2016 | 07:40

Kuno kwa Chilinde tikuthokoza chifukwa chotikonzera nseu wochoka pa Parish, achite chimodzi modzi ndi miseu yina yofunika kupala

Nseu Chimwankhunda

18-Aug-2016 | 06:41

Bwana MP atithandize kuno ku Chimwankhunda nseu wopita ku chihema nkale adalonjeza atikonzere

Kukonza Mseu kwavuta

18-Aug-2016 | 13:58

Kuno kwa Senti chitukuko cha mseu sichikuyenda bwino

Kuima kwa ntchito yokonza mseu kwa Senti

18-Aug-2016 | 17:10

kuno kwa Senti pali vuto lokonza mseu, pakuoneka kuti pali kukokana nde zaima

AREA 49 Nseu Wopita pa Mvama

20-Aug-2016 | 10:02

Mutikozeleko Nseu ku 49 wochoka pa Zebra stage kulowa nkati kupita pa Mvama Church

Area 25 Nseu wa Dzenza *Resolved*

09-Jun-2016 | 10:15

KUNO ku 25 nkhani ndi ya msewu wa Dzenza suli bwino. Akanapanga machawi nkhani yokonza msweu umenewu

Project yomalizitsa Kumanga Nseu Ikuchedwa

20-Aug-2016 | 07:35

Kuno kwa Senti project yomanga nseu ikuchedwa chifukwa cha ndale

Ntchito Yokonza Mseu Kwa Senti

15-Aug-2016 | 12:08

Kuno kwa Senti Pali kulozana zala zakuima kwa ntchito yokonza MSeu.

Kuthokoza Khansala Pokonza Mseu

22-Aug-2016 | 08:31

kuno ku ntandile tithokoze khansala poika ma ring mu nseu

Kuno Kwa Senti Project Ya MSeu sikulongosoka *Resolved*

17-Aug-2016 | 10:14

kuno kwa senti tikudandaula project ya mseu yosalongosoka

Achite Machawi Pokonza Miseu

19-Aug-2016 | 10:22

Kuno kwa Mtsiliza tiyamike dongosolo loika ma ring mu miseu koma pakufunika madera onse zitheke nthawi ya mvula isadafike

Fumbi lachuluka Achitepo kanthu

11-Jul-2016 | 17:05

Kuno ku 25 nsungwi kuri fumbi chonde azitithirira madzi mmisewu