Atikonzere Miseu ku Kafukule

26-Feb-2018 | 09:02

Kuno ku Kafukule miseu yobwera pa msika waukulu sili bwino akonze ngati kuchoka kwa Chuyu, chinyera ndi mphimbi

Vuto la Mseu ku Mimosa

09-Feb-2018 | 16:02

Kuno ku Mulanje Mimosa. Pempho ndi loti atipalire mseu kuchoka pa Mimosa kufika pa msika wa Chikuse. Mayendedwe monga kwa anthu ochoka kwa Nkhonya amavutika.

Mponda Road Area 3

25-Jul-2018 | 07:41

Council should consider maintenance

Request to do maintenance work on Malangalanga-Forz road

14-Jun-2017 | 11:07

We would like to request the council to consider patching potholes on the road between the turn by Malangalanga and Forz.

Well Done City Council

19-Aug-2018 | 07:26

I would like to express my appreciation to Lilongwe city council for works on the road at the turn in Forz from Malangalanga. We had complained for so long

Atikonzere Mseu ku Shire

01-May-2018 | 16:02

Kuno ku Area 49 Shire tili ndi pempho loti atikonzere mseu wa pa turn ya stage kulowera ku Tilinanu orphanage.

Atikonzere Nseu Wa pa Kakule School

02-Jul-2018 | 08:23

Chinsapo pempho nali. Atikonzere nseu wopita ku Kakule primary school

Atikonzere Mlatho

25-Mar-2018 | 06:49

Kuno kwa Senti tikupempha kudzera mwa Khansala wathu kuti atikonzere mlatho wopita pa Mkombaphala

Pa Zokambirana Za Miseu

26-Aug-2018 | 18:38

Ine ndati ndithirepo ndemanga program ya lero. Zoonadi ndibwino anthu tiziziwa chonchi kuti kodi ma contractor amasankhidwa bwnanji. Zitha kukhala kuti apa akungolongosola komabe chinyengo chilipo.

Comment on Mzinda Radio Program

26-Aug-2018 | 17:57

I would like to share a comment with regards today's program. I think the director of engineering in saying there is transparency in selection of contractors and that several outsiders who are professionals are involved might not necessarily guarantee a good job. From what he said interms of staffing at the council, thats what I think is the problem. I don't on his own he can be able to supervise all projects. The council needs to recruit more engineers.

Mseu wa Don Bosco atikonzere

14-Aug-2018 | 11:58

area 23 tsabango 2 mseu wadon bosco please tikozereni akhasala. Komanso escom ndi water board akuyenjeza

Atithandize ndi mlatho kuno ku Solzbery lines

30-Jun-2018 | 17:35

Tati tipempheko kuti atithandize ndi mlatho kuno ku Solzbery lines mzuzu. Komaso tikapita ku health center amachedwa kutithandiza