Pempho kuno kwa Chinsapo

21-Jul-2016 | 09:19

Madzi ndi misewu ndiyovuta kwachinsapo

Tiyamikire Atsogoleri Athu

29-Aug-2016 | 08:48

Ndati ndiyamike atsogoleri athu kuno ku Area 25 Kabwabwa ward pokonza dongosolo lopala nseu wopita ku Chiuzimba

Pempho loti atipalire nseu ku Nsungwi Area 25

30-Aug-2016 | 13:04

atipalireko nsewu kuchokera pa conner ya 49 mpaka pa famers world kunsungwi kuno ku 25

Ndirande Malabada Atipalire Nseu

03-Sep-2016 | 10:10

Kuno ku ndirande malabada atsogoleri athu alinganize dongosolo lopala nseu wochoka pa nsika suli bwino

Tithokoze atikonzera Bridge ya Chiwoko

05-Sep-2016 | 10:02

tithokoze atsogoleri athu kuno ku Area 38 potikonzera bridge ya Chiwoko..

Pempho kwa anthu ku Area 36

06-Sep-2016 | 06:47

Ndati ndipempheko anthu aku Area 36 kuti pamene akukonza nseu wa Kandikole ena akumabweranso kuzachosa miyala ya quary kukagulisa. dera litukuka bwanji chonchi

Bangwe Atikonzere Nseu *Resolved*

08-Sep-2016 | 09:10

atikonzereko nseu kuno ku bangwe wochoka pa nzikiti ku Namatapa kupita njira ya ku manda

Pempho Kalambe Ward

18-Sep-2016 | 08:12

Kuno kwa mngwangwa kwa T/A Kabudula timasowa msewu wabwino ndi chithandizo cha msika wabwino. Zikomo

Watinozgere Mseu pa Kapamba

06-Oct-2016 | 07:41

kuno ku chibavi pa kapamba mseu uli makora cha

Yankho pa pempho lokonza mseu

06-Oct-2016 | 17:20

tikonza mseu umenewu pempho lanu tiliona na bwana mp. P Ngoma

Tiyamikire atsogoleri athu

06-Oct-2016 | 13:05

Ine chembekezo chaiwalika ndimakhala m'mudzi mwachankhoma ku area36. ndati ndiyamike kuti Akhasala athu AStela khumula ndi bwana MP AMasi akutithandiza pa vuto la madzi ndi misewu yomwe inali yoipa.

Pempho kuno ku Area 24

16-Oct-2016 | 09:37

Area 24 mavuto ndi ambiri tiuzileni a MP zamavuto aza madzi, miseu mijigo ndinso ESCOM nkhani ya magetsi. t