Area 36 Atikonzere Mlatho *Resolved*

07-Jul-2016 | 19:45

Ife tinene zaku 36 Phwetekere ward msewu nde uli bwino koma nkhani yina cha nkati kwa chumba atikonzere mlatho pa Nsambeta

Mlatho Chitawira Blantyre

09-Aug-2016 | 05:50

chitawira bwana MP akonze mlatho wa pa mlambalala kupita ku ntonya

Atikonzere Mseu wa Ngwenya *Resolved*

08-Aug-2016 | 08:24

khansala wathu ku Ngwenya adalonjeza mseu sukukonzedwa mpaka pano

Road to Kakule Primary

09-Aug-2016 | 15:12

Ku Chinsapo 2 atikonzere nseu wopita ku Kakule primary school. Mayi Loga. Business Woman

Fruits of MASAF Phase 4 Project

12-Aug-2016 | 11:59

Residents of SESE ward in Lilongwe are today fixing rings at Tongole Bridge in the area. Councilor for the area Frank Lebian says they will also do the same in nsinje and mchitanjiru areas in the ward. Share with MZINDA a report on developments in your area

Nseu wa Nazarene

13-Aug-2016 | 08:17

Bwana MP kuno ku Bangwe athire dothi nseu wochoka mutala kupita pa Nazarene. SAULOS WOMETA

Atikonzere Nseu wa Salima

22-Aug-2016 | 20:40

Kuno ku salima msewu wathu sulibwino,okumbika komaso ndiwaung'ono kuchokera ku salima depot kupita ku sengabay Livingstonia,road signs ulibe koma ndiomwe umakhala busy nthawi zonse.tithandizeni pliz.Ine Richard katengeza,ngolowindo village,TA maganga

Area 23 Nseu wopita ku Don Bosco

21-Aug-2016 | 16:20

Kuno ku Area 23 bwana MP ationereko nseu wopita ku Don Bosco.. tikuthokoza adathira miyara malo ena koma ena sadathire. tikuopa kuti nthawi ya mvula ikafika nseu uzavuta

NSEU

05-Feb-2021 | 10:52

nseu opita ku gologota dela la 23 siwabwino, boma lipangepo kathu pakhani yatala.

Vuto la Mseu ku Mimosa

21-Aug-2018 | 14:58

Kuno ku Mulanje Mimosa. Pempho ndi loti atipalire mseu kuchoka pa Mimosa kufika pa msika wa Chikuse. Mayendedwe monga kwa anthu ochoka kwa Nkhonya amavutika.

Phwetekere Ward Atikonzereko Nseu

17-Aug-2016 | 16:32

area 36 nseu wochoka pa mbukwa kupita pa tank akonze. wakumbika kwambiri

Kwa Senti Atikonzere Mlatho

19-Aug-2016 | 11:24

Kuno kwa Senti tikupempha kudzera mwa Khansala wathu kuti atikonzere mlatho wopita pa Mkombaphala