Bin ya pa Msika wa Nayizi yadzadza

05-Feb-2017 | 05:18

Bin yathu kuno ku NAYIZI pa Msika yadzadza, chonde abwere kudzachotsa

Improvement in Power Supply

01-Feb-2017 | 08:42

I would like to commend ESCOM for the improvement in power supply here in Area 23. Great work team ESCOM.

Vuto la madzi ku Area 23

01-Feb-2017 | 08:37

kuno ku 23, dera la gologota, madzi akuvuta kwambiri, akumatuluka kamodzi kapena kawiri pa sabata.

Tiyamikire kuyaka kwa magetsi kuno ku Chikwawa

31-Jan-2017 | 03:26

Ife Kuno Kuchikwawa T/A Chapananga V/G Lackson Mudera Mwathu Magetsi Alipo ndipo amayaka bwino Ine F.Stephano.

Waste Collection a challenge in Nkhotakota

30-Jan-2017 | 17:45

There is an accumulation of waste at Mwansambo Trading. The picture shows our worst disposal pit, it is very close to main road just as you seen students are passing by. The Assembly needs to do something about this

Awareness on planting trees a welcome development

30-Jan-2017 | 03:55

Let me commend our Councilor for Misesa ward Louis Ngalande for being part of the big walk organized to raise awareness on the importance of planting trees. This is a welcome initiative.

Power is a persistent problem here in Machinjiri

30-Jan-2017 | 03:19

My name is Peter Kamama,from Khama Machinjiri, I would like to report that our biggest problem is power. We usually have supply only thrice a week.

Ma pipe ena amadzi sakulimba

28-Jan-2017 | 18:03

Kuno ku chilomon tili ndi vuto lophulika phulika kwa ma pipe zomwe zikupangitsa kuti mazi azisowa

Pempho kwa anthu akuno ku Zingwangwa

28-Jan-2017 | 10:11

Kuno ku Zingwangwa anthu tikuchulutsa umve kutaya zinyalala paliponse. Chonde tatiyeni tisinthe. Ine Saidi

Pa Msika waukulu ku Mbayani palibe Bin

28-Jan-2017 | 09:07

Pa Msika waukulu ku Mbayani palibe Bin. Kotero anthu ena amakataya zinyalala ku njanji komanso malo ena zomwe zimaika chiophyezo pa miyoyo yathu

Vutu lakuzima kwa magetsi

28-Jan-2017 | 07:28

Kuno ku Zomba kwa Mpondabwino tili ndi vuto lakuzimazima kwa magetsi. Ine Lemusi Kawanga

Kagwiridwe ka ntchito pa chipatala cha Mbayani

28-Jan-2017 | 06:15

Kuno Ku Mbayani, Pa Chipatala Chathu Pali Vuto Loti Mma Week End Sipagwilidwa Ntchito Molongosoka, Mwa Chitsanzo Munthu Ngati Wadwara Loweruka Madzulo Uyembekezere Kuthandizidwa Loremba.Tithandizeni Vuto Limeneri. Ine Stan Kazoma.

Msika wa Mbayani ulibe Bin

28-Jan-2017 | 04:07

Zinyalala anthu angotaila paliponse kuno ku Mbayani chifukwa pa Msika wathu waukulu palibe Bin.AGATHA PADDY

Magetsi akuvuta kwambiri kuno ku Mbayani

28-Jan-2017 | 04:07

Magesi akuvuta kwambiri kuno ku Mbayani. Ndine ulemu majiga

Vuto la madzi kwa Gayesi

28-Jan-2017 | 04:07

Kuno ku Mbayani madzi akumasiyasiya m'maka kwa Gayesi.

Kuyamikira aziphunzitsi apa sukulu ya Nkolokoti

27-Jan-2017 | 11:41

Ine monga m'modzi mwa kholo lomwe lili ndi mwana wa sukulu pa Nkolokoti ndati ndiyamikire khama la aziphunzitsi apa sukuluyi