Atiganizire pozayika chi bin pa msika wa Mbayani

26-Jan-2017 | 14:17

Zinyala zikuvuta potaya Bin tilibe pa msika kuno ku Mbayani

Atikonzere mseu kuno ku Area 25C

26-Jan-2017 | 09:29

Ndati ndipemphe nawo kuti mseu wopita ku Mtunda ku Area 25C New vision suli bwino ngati kungatheke atithilireko dothi

Madera ena akufunika ma pipe amadzi anyowani

26-Jan-2017 | 08:20

Ndati ndipemphe nawo ku Water Board ya Blantyre kuti pali ma dera ena kuphulikaphulika kwa ma pipe amadzi ndi chifukwa chakuti ma pipe ena akhalitsa osati anthu kuononga kotero ngati kuli kotheka ku malo koteruku abweretse ma pipe anyowani ngati kuno ku Mzedi

Request to collect garbage in Area 47

26-Jan-2017 | 07:49

There is a heap of garbage close to st johns covenant school in sector 3 area 47..therefore making the road to be narrow and a problem to parents picking up their school kids, can our Councillor intervene on this

Problems that we experience in Chilomoni

26-Jan-2017 | 07:41

I would like to report that the main problems that we experience here in Chilomoni are water and electricity. service delivery in these two ares is not so good

Pempho kwa anthu anzanga kuno ku BCA

26-Jan-2017 | 00:40

Ndati ndipemphe anzanga kuno BCA komanso Namiyango kuti mwapadera tatiyeni kumbali ya ukhondo aliyense atengepo gawo komanso pamene tadziwa zanjira yina yotilumikizitsa ndi atsogoleri athu ya Mzinda, tatiyeni tigwiritse bwino ntchito

Tikupempha nawo nseu watala kuno ku Namiyango

26-Jan-2017 | 00:04

Kuno kunamiyango tikupempha nawo nseu watala ngati anzathu ku Mthandizi

Pempho kuno ku Masala Bangwe

25-Jan-2017 | 17:04

Kuno ku Masala Bangwe tiyamikire kuti pakatipa magetsi akhala akuyakako bwino koma vuto la madzi nde likupitilira

Atikonzere mseu kuno ku Chiputula

25-Jan-2017 | 17:01

Kuno ku Chiputula ku Mzuzu mseu suli bwino. Tipemphe nawo khansala wathu kuti atithandize

Tiyamikire Khansala wathu Namiyango Ward

25-Jan-2017 | 16:59

Kuno ku Namiyango ndati ndiyamikire Khansala wathu ntchito akugwira bwino limodzi ndi mafumu. pokhala pofunika zokambirana amayitanitsa anthu pa sukulu

Sabata imeneyi magetsi ayaka bwino kuno ku Bangwe

25-Jan-2017 | 12:15

kuno ku Bangwe vuto linali kuthima kwa magesi koma sabata yathayi zinali bwino

Blantyre Water Board ibwezerese ofesi ya Bangwe

25-Jan-2017 | 11:43

Ndati ndipemphe nawo Blantyre Water Board kuti ngati kuli kotheka abwezeretse ofesi yawo pa Bangwe. M'mene kanalipo ka ofesi kameneka kunali kosavuta kwa ife kupita ndi mavuto athu

Pempho kwa anthu aku Bangwe Mthandizi

25-Jan-2017 | 10:58

Ndikupempha anthu aku Bangwe Mthandizi ward kuti tatiyeni tonse tigwirane manja pa nkhani za chitukuko posatengera kuti mzanga ndi wa chipani chanji. Ife monga atsogoleri tili konzeka kumva dandaulo la wina aliyense. Zikomo. Cllr Ramsey Gomani

Ku Chilomoni kwa Nthukwa Msika ukuchepa

25-Jan-2017 | 10:40

Ife kuno Ku chilomon kwa nthukwa tufuna mutikonzere msika wathu ukuchepa. ine Samuel salema

Request to Blantyre Water Board

25-Jan-2017 | 09:50

I write to request the Blantyre Water Board to ensure means are in place that can make us consumers be sure that someone is indeed a member of staff of BWB because imposters are also out there. I would propose that each area such as Bangwe should have some two or three specific people to whom we can be introduced and know that it is these through which we will get assisted

Achitepo kanthu nkhani ya mseu kuno ku Namiyango

24-Jan-2017 | 00:05

Kuno ku namiyango mseu wathu sulibwino ayi. achitepo kanthu