See attached a notice from the Lilongwe Water Board on the second phase of the house to House Survey and Meter Validation Exercise
We would like to request the council to consider patching potholes on the road between the turn by Malangalanga and Forz.
Ine Aaron kuno ku Namiyango ndikuyamika Khansala athu komanso akhonsolo pa chitukuko chokonza msewu kuchoka pa weaving kuzungulira ku church cha CCAP mpaka pa Caltex.
I am not happy with the way Escom is rendering its services here. It is selective in its way of providing new connections. Some have been given the power, while some of us feel sidelined. On the same grid, others have been connected.Concerned citizen in Area 44.
Ine ngati m'modzi mwa anthu akuno ku Ndirande Makata ndati ndiyamike ntchito yabwino yomwe akugwira akhansala athu Mayi Cecilia Zeka Phiri. Komanso ubale wawo ndi phungu wathu kuno.
Monga mmene mungaonere mu chithuzi ndaika apache kagwiridwe ka ntchito pa msewu wa magalasi sikakuyenda bwino. Msweu uli mkati pokonza koma mbali yomwe agwirako kale kwaonongeka nthawi yomweyi.
Kuno ku Ndirande Makata tili ndi pempho ku Khonsolo kuti atibweretsere ma skipper mmaka pa nsika waukulu. Ukhondo palibe. Ine Naomi Sunduza
Kuno ku Chilomoni vuto lomwe tili nalo lalikulu ndikuvuta kwa madzi. Nthawi zambiri masana onse sitikhala nawo amatuluka usiku okha
Nancholi area around the main market we have not had water supply since sunday afternoon. Would they please assist us.
Tikumwabe madzi a pa chitsime mpaka lero. Timatsekula mmimba pafupi pafupi. Chonde tithandizeni, amati sangatipatse mjigo poti tili dera la mu mzinda, koma madzi a mpope sanafike mpatali ndi ma paipi tokha sitingakwanitse. Tili mmalire a Masasa ndi Msongwe. Dera la mfumu yaing'ono Chifwayi. Mabanja okhuzidwa kwambiri ndi banja la Mphande, Kaira, Chirwa ndi Kaunda. Chonde fufuzani nkhaniyi tisafe ndi kolera boma lilipo. Ine ndi Jailos kaira 0881451910
Kuno ku Mtandire anthu abwereranso ku malo omwe analetsedwa ndi boma Kamba ka madzi anasefukira aja. Apa m'mene ateremu nde kuti zitati zichitikenso anthuwa azavulala kwambiri. Chonde alowelelepo ndikukonza zoti malo ena oti anthu nkukhala apezeka.
NOTICE OF WITHDRAWAL OF PROVISIONAL OFFERS FOR PLOTS AT KATOTO AREA 6. Mzuzu City Council (MCC) wishes to inform those that were provisionally offered plots at Katoto Area 6 that, with mandate from the Plots Allocation Committee, it will withdraw all plots that will not have fully been paid for by June 10 2017. This is because the period stipulated in the provisional offer has expired. To avoid withdrawal and re-allocation of the plots, those who were offered the plots should pay the development fees by the stated date to the following bank details: Account number: 0005704000200 Account name: Mzuzu City Council Development Account Bank: First Merchant Bank Branch: Mzuzu Proof of payment should immediately be submitted to the Planning Department’s estates section. Those who finished payment but have not collected their formal offers of allocation should do so from the Planning Department situated at Mzuzu Stadium upon production of proof of payment. Those who finished paying should also submit building plans to Mzuzu City Council Town and Country Planning Committee for approval within 90 days from the date of offer. Meanwhile, MCC is inviting applications for plots for both high and medium density housing at Area 6 Extension. Applications should be submitted along with specifications for preference to the Planning Department. For details, contact the undersigned on 0999491976 or Tina Nyirongo on 0994773349 or 01325000. Gift Grace Lungu (Estates Management Officer) FOR: THE CHAIRMAN, PLOTS ALLOCATION COMMITTEE
Kuno ku Namiyango tati tipemphe nawo kuti atsogoleri athu akamapanga ma plan achitukuko atiganizire mbali ya nsewu kuchoka pakona pa 4 ways kudutsa pa Tondole mpaka kunsika
There is a leakage on our meter here in Area 1. The house is in the name of Kaonga next to Centurion bar. A plumber came to replace the previous meter we had and it seems it wasn't properly done.
On behalf of the people from Dowa, Bowe area to be specific I would like to send out a request for a new police unit for the area. The current station as you can see in the attached picture is terrible.
New Gulliver Area 49 has had no water supply for 5 days now. We took note of the interruption notice but it indicated that there would be no water supply on Friday only.