Dandaulo pa kagwiridwe ka ntchito pokonza msewu wa Ndirande magalasi
Monga mmene mungaonere mu chithuzi ndaika apache kagwiridwe ka ntchito pa msewu wa magalasi sikakuyenda bwino. Msweu uli mkati pokonza koma mbali yomwe agwirako kale kwaonongeka nthawi yomweyi.