Request to expand Luwinga market

24-Jul-2017 | 08:51

I would like to request authorities, be it the councillor for Luwinga ward or officials at the council to look into areas in which people ply their trade in community markets. I was passing through the market at Luwinga and took not that some women are selling sugar cane just close to where there is a bin. Apparently they say they were told that there is no place for them in the market. When you look at the picture you will understand that this is a healthy hazard. Whatever action can be taken, please it should be taken.

Vuto la madzi ku Bangwe

24-Jul-2017 | 06:02

Kuno ku Bangwe vuto la madzi likupitilira. Nthawi zambiri madzi akumasiya kopanda kutidziwisa.

Kuonga pa chitukuko cha mseu

24-Jul-2017 | 05:15

Kuno ku Mchengautuba tikuonga khansala withu chifukwa cha mseu

Request for clinic in Chiputula

24-Jul-2017 | 04:57

I would like to request through our councillor and for the attention of all those responsible that they should considered giving us residents of chiputula a small community clinic. Right now people travel long distances to the main Mzuzu hospital

Vuto la madzi ku Chilinde

24-Jul-2017 | 04:46

Kuno ku Chilinde 1 madzi akusiyasiya ndipo ife azimayi tikulephera kugwira zintchito zina chifukwa tikukhalira ku chitsime. chonde chonde atayesesa kasiyidwe kachepe

Fumbo pa ma sanitation rooms pa msika wa target

23-Jul-2017 | 16:55

Tati tifumbeko khansala withu kuti ka ma sanitation rooms ayo wali kuzenga na ovwiri wa Plan pa msika wa Target yajulikenge pa uli. Chifukwa process ya kuzenga ikuoneka kuti ili kumalika nikale.

Tukhumba Clinic kuno ku Chiputula

23-Jul-2017 | 09:32

Kuno ku chiputula ward ku Mzuzu tukhumba kuti watipe clinic. Kwa sono wanthu wakwenda long distances kuluta ku boma mwakuti ma referral tupangira pa CBO

Dumping of rubbish behind Mzuzu Shopryt

22-Jul-2017 | 11:35

Rubbish is being dumped just behind Mzuzu shopryt and its accumulation is posing a health hazard to users of the road close by and people leaving in the nearby locations. The City Council should intervene

Sugzo la Unkhungu ku Katawa

21-Jul-2017 | 16:52

Kuno ku Katawa kuli suzgo lakuti para wanthu wakoleka kuti wali kwiba vinthu nakuluta kupolice wakuchedwa yayi kufuma. So para ivi vikuchitika tingalutaso nkhu.? ka uko tikumanya kuluta na ma suzgo aya ni ku police

Atitsegulire Water Kiosk kuno kwa Ching'ambo

21-Jul-2017 | 12:41

Kuno ku Zolozolo west kufupi na Chiputula pali ka water kiosk kanyakhe kali kujalika kweni wanthu tiliko wanandi mwakuti tikusuzgika kutheka maji.

Kuzimwa kwa Magesi ku Mzilawayinge

21-Jul-2017 | 11:29

Kuno ku Mzilawayingwe suzgo ni kuzimwazimwa kwa Magesi. Ka pali kukondera kuti uku wazimenge chomene kujumpha kunyake? Wanyithu pa Katawa penipapa yakuzimwazimwa yayi

Non collection of waste at Mwenyekondo market

21-Jul-2017 | 10:33

I wish to report that waste has accumulated at the Bins close to Msonkhamanja CCAP. Why is it that they always seem to wait for things to reach this level?

Kunangika kwa Mseu pa Lunyango

21-Jul-2017 | 09:35

Mseu uli kunangika chomene pa Lunyango ku Zolozolo wets. Ma galimoto yangajumpha yayi nakuti tikusuzgika kujumphapo na walwali

Dandaulo pa Mseu wa ku Chiputula

21-Jul-2017 | 08:41

Ndati ndifunse nawo kuti kodi program yokonza mseu wa Chiputula wodusa pa four ways itha liti. Anthu tikudandaula kuti ukuchedwa

Fumbo pa Water kiosk kwa Msonda

20-Jul-2017 | 16:54

Kuno kwa Msonda Mchengautuba west tati tifumbe nawo kwa Khansala withu na ku water board kuti ka Water kiosk watipinge pa uli

Kwa Dekezga ma Latrine kulibe

20-Jul-2017 | 12:29

Kuno kwa Dekezga Masasa ward tikufuna ma latrine ngati amene ali kwa Geza mugomo