Pempho kuno ku Area 24

16-Oct-2016 | 09:37

Area 24 mavuto ndi ambiri tiuzileni a MP zamavuto aza madzi, miseu mijigo ndinso ESCOM nkhani ya magetsi. t

Atthandize ndi mjigo kuno kwa Chimoka

19-Oct-2016 | 05:24

kuno kwa senti kwa chimoka tufuna mjigo. Ine mayi mnjedza wa thobwa

Lilongwe Water Board Water Rationing Schedule

17-Oct-2016 | 08:37

Remember LWB reservoirs (Kamuzu Dam I and II) are fast being depleted. Always use a bucket, pail, cup, not running water to wash clothes, utensils, brush teeth. SMS LWB to 253 for updates on the water situation.

LILONGWE WATER BOARD WATER RATIONING FROM MONDAY 24/10/16

23-Oct-2016 | 13:40

Water Rationing Schedule for week beginning Monday 24th October to Sunday 30th October, 2016. Remember although we are doing all the best to save the little water that we have, LWB reservoirs (Kamuzu Dam I and II) are fast being depleted. Always use a bucket, pail, cup, NOT running water to wash clothes, utensils and brush teeth.

Pempho Nankhaka Ward

02-Nov-2016 | 03:20

Kuno Ku Nankhaka Wodi T/A Chitukula Tili Ndimavuto Awa Madzi Komanso Magetsi Koma Zonse Tinapanga Kale Apulayi Komano Magetsi Anatiuza Kut 24milion Kuchokela CP Kufikila Pa Chitukula T/C Ndikupepha Mabugwe , Aboma Ndi Ena Onse Akufuna Wabwino Kuti Atithandize Zikomo.

Kuvuta kwa madzi

05-Nov-2016 | 08:59

ine dzina langa Ofesi ndimagwira ngati guard pa Kanjala motors vuto liliko kuno ku Chilinde ndi madzi. pilizi chonde zithe

Madzi avuta kwambiri kuno ku Mchesi

04-Nov-2016 | 18:14

kuno ku Mchesi madzi akuvuta kwambiri, ine monga m,modzi mwa osewera mpira mu timu ya Bekery zikumandivuta kusamba tikachoka kusewera mpira titada koma kupeza madzi asiya

Kuno ku area 24 madzi akusiyasiya

03-Nov-2016 | 13:22

madzi akusiyasiya kuno ku 24...

Mavuto omwe tili nawo kuno ku Kasungu

06-Nov-2016 | 16:31

Ndimamvera programe ya Mzinda pa Zodiak, ngakhale ife kuno ku Kasungu sitirinawo pa Project yanu, komabe mutifikisire mabvuto amane tikukumana nawo kuchokera ku ESCOM ndi Central region water board. 1. ESCOM, magesi amangozimazima tingoti mwina pa week timakhala ndi magesi kwa nthawi yokwana 8 hours koma ma bill akumakhala okwerabe, tikafusa za ma prepaid meters amati amayikira ku ma meter amene ali ndi fault koma tikapitiriza kuti za m'mene amaziwira kuti meter iri ndi fault amati anzanu amapereka ndalama not less than k10'000 kuti zitheke. is this true? 2.Water board, madzi amaturuka usiku okha every 2weeks

Pempho kuno kwa Chinsapo

21-Jul-2016 | 09:19

Madzi ndi misewu ndiyovuta kwachinsapo

LILONGWE WATER BOARD WATER RATIONING FROM MONDAY 07/11/16

07-Nov-2016 | 05:44

Water rationing schedule week beginning 7th November, 2016. Remember: Always use a bucket, pail, cup, NOT running water to wash clothes, utensils and brush teeth.

LILONGWE WATER BOARD INTRODUCES ON-SITE BILLING

07-Nov-2016 | 14:40

PILOTING OF THE ON-SITE BILLING SYSTEM (POMPO-POMPO BILLING) Lilongwe Water Board (LWB) is pleased to inform all its valued customers that it will soon be rolling out its Pompo-Pompo Billing Service that will enable meter readers to read meters using mobile devices, bill and print the bill slips right on site soon after the meter readings have been captured. To enable a smooth transition from the current system to this on-site billing and printing system, the Board embarked on the pilot phase of the project from Monday 7th November, 2016. The areas involved in this pilot phase include: Area 18 in the Northern Zone; Areas 15 and 41 in the Central Zone; and Areas 37 and 38 in the Southern Zone. The Pompo-Pompo Billing Service is one of the reform areas in the on-going Malawi Government’s Public Sector Reforms Management and is expected that once fully rolled out, the service will enable the Board to reduce the challenges it faces in the delivery of water bills to its customers and help the Board’s customers plan appropriately when settling their bills. The Board is appealing to all its customers to support the meter readers as they undertake the exercise. Once the service is fully implemented, it will also enable customers to get water bills on their mobile phones through an SMS, therefore, during the meter reading customers will also be requested to provide their mobile phone numbers that will be logged into the system. The Board further appeals to its valued customers that whenever they have queries over their bills, such queries should be brought to the attention of the Board through the Zone Offices or the Head Office for redress and not directly to the meter readers on site. Help Lilongwe Water Board to serve you better MANAGEMENT