Vuto lakusiyasiya kwa madzi

26-Jan-2017 | 16:07

Kuno ku Mbayani limodzi mwa mavuto omwe tili nawo ndi kusiyasiya kwa madzi. Ndine Maggie Chirwa

Ma pipe ena amadzi sakulimba

28-Jan-2017 | 18:03

Kuno ku chilomon tili ndi vuto lophulika phulika kwa ma pipe zomwe zikupangitsa kuti mazi azisowa

Vuto la madzi kwa Gayesi

28-Jan-2017 | 04:07

Kuno ku Mbayani madzi akumasiyasiya m'maka kwa Gayesi.

Vuto la madzi ku Area 23

01-Feb-2017 | 08:37

kuno ku 23, dera la gologota, madzi akuvuta kwambiri, akumatuluka kamodzi kapena kawiri pa sabata.

Report on burst water pipe Area 49 Lilongwe *RESOLVED*

06-Feb-2017 | 04:20

I'm writing to report of a burst water pipe here in Area 49 Baghdad on Chimdidi street. Water is just spilling out.

Kuphulika kwa pipe ya madzi *RESOLVED*

17-Feb-2017 | 13:47

Pipe ya madzi yaphulika ndipo madzi akutaika kwambiri kwa Kachere cha kufupi ndi kwa Kambuzi. Mai Chilundu

Kuyamikira katulukidwe ka madzi

19-Feb-2017 | 13:03

Kuno ku Area 49 Dubai ndati ndiyamikire katulukidwe ka madzi masabata awiri apitawa. Ndipo ndipemphe kuti izi zipitilire

Pempho la mjigo kuno kwa Chimwanya

03-Mar-2017 | 17:07

Kuno kwa Chimwanya ku Lilongwe tikupempha nawo atsogoleri athu kuti alingalire zotipasa mjigo wina, dera lonse mjigo ndiumodzi ndipo ambiri mwa ife timayenda ntunda wautali

Notice from Blantyre Water Board

10-Mar-2017 | 19:13

Tomorrow, 11th March 2017, from 8am to 5pm, there will be no power at Mudi Works Pumping Station. ESCOM will be commissioning the newly installed power line at Mudi Station. This will result in no pumping at all and customers in Limbe Zone will have low pressure or no water during this period. Customers are therefore being advised to store enough water and use it sparing until works are completed. We apologise for any inconvenience this may cause. Water is Life, Conserve it

Kuvuta kwa madzi ku Machinjiri

17-Mar-2017 | 14:10

Kuno ku Machinjiri kwa Mkwate madzi akusiyasiya kulekana ndi madera ena ku Machinjiri konkuno, kodi ichi ndi chifukwa chachani

Pempho la wáter kiosk ku Ndirande Zambia

17-Mar-2017 | 15:09

Ndati ndipemphe kuti ife kuno ku Ndirande Zambia timasilira anzathu ku Makata ali ndi wáter kiosk yabwino pa Khoza pamene ife kuno kulibe. Kodi mabungwe omwe adathandizapo za Project imeneyi kuno sangafike?

NOTICE FROM BWB

17-Mar-2017 | 18:17

Technicians are still working on a 450mm pipe burst fault in Kwacha Central Area. Therefore, Chinyonga, Kanjedza and other areas in Limbe will continue to experience no water until the problem is resolved. We will keep you updated.