Kuno ku Ndirande makata kufupi ndikomwe kuli water kiosk ya Khoza pipe ya madzi yaphulika.
Madzi kuno ku Mchesi akasiya akumakonda kuyamba usiku, bwanji muzitipasako masana kuti tizitunga nthawi yabwino
The water pipe reported broken was fixed
There is a burst water pipe off Chinyonga stage. Water is spilling out heavily.
Water rationing schedule week beginning 14th November, 2016. Remember: Always use a bucket, pail, cup, NOT running water to wash clothes, utensils and brush teeth.
Kuno ku Masasa suzgo ilo tili nalo ni magi. please chonde watiwvire
Kuno ku Masasa maji ayo tikumwa yali makora yaye. watowvire na Mjigo please
kuno kumasasa maji yakusuzga
Kuno ku Chasefu suzgo ni maji kulekaleka
Suzgo ni madzi akumwa kuno ku Geisha timatunga pa kachitsime koti sikasamalika
Kuno kumasasa vuto ndi madzi. madzi abwino a-Water board sanabwere komanso mjigo kulibe timatunga pa ka chitsime kosakhala bwino
Water Rationing Schedule for Week beginning Monday 21st November 2016. We really appreciate for your support and understanding.