Chilomon ward, New namiwawa near top lodge. Pipe ya madzi inaphulika week yatha kupanga report akungoti abwera koma madzi akutaika kwambiri
Michiru area after Sonke's junction behind mbiridzi's residence. Two pipes on same road akutaya madzi mochuluka
Kuno ku Area 24 pafupi ndi panyenye stage pipe ya madzi ya water board yaphulika
Kuno ku mamiyango vuto ndi madzi ndi magetsi komanso miseu silibwino
Kuno ku Masala Bangwe tiyamikire kuti pakatipa magetsi akhala akuyakako bwino koma vuto la madzi nde likupitilira
I write to request the Blantyre Water Board to ensure means are in place that can make us consumers be sure that someone is indeed a member of staff of BWB because imposters are also out there. I would propose that each area such as Bangwe should have some two or three specific people to whom we can be introduced and know that it is these through which we will get assisted
Ndati ndipemphe nawo ku Water Board ya Blantyre kuti pali ma dera ena kuphulikaphulika kwa ma pipe amadzi ndi chifukwa chakuti ma pipe ena akhalitsa osati anthu kuononga kotero ngati kuli kotheka ku malo koteruku abweretse ma pipe anyowani ngati kuno ku Mzedi
Ndati ndipemphe nawo Blantyre Water Board kuti ngati kuli kotheka abwezeretse ofesi yawo pa Bangwe. M'mene kanalipo ka ofesi kameneka kunali kosavuta kwa ife kupita ndi mavuto athu
Kuno kwa Kachere tati tipemphe kwa a-Water Users Association kudzera mwa Blantyre Water Board kuti apange chotheka kiosk ya m'mudzi mwa Andulu iyambenso kugwira ntchito. Ine Cosmas Chamveka
Ma paipi amadzi ambili anthu akumaononga mosavuta chifukwa ena ndi aplastic sangapange dongosolo loti onse akhale achitsulo?
Ndati ndikambe nawo kuti kuno kwa Kachere madera ena madzi amasiya nthawi yaitali pamene kwina kwa kanthawi kochepa. kodi ichi ndichifukwa chani
I would like to report that the main problems that we experience here in Chilomoni are water and electricity. service delivery in these two ares is not so good