Ku Geisha madzi akumwa sali bwino

19-Nov-2016 | 14:58

Suzgo ni madzi akumwa kuno ku Geisha timatunga pa kachitsime koti sikasamalika

Kuno ku Masasa Maji ayo tikumwa mbawemi cha

19-Nov-2016 | 14:57

Kuno ku Masasa maji ayo tikumwa yali makora yaye. watowvire na Mjigo please

Tiwonge kuno ku Jombo ward

19-Nov-2016 | 14:56

Jombo ward Khansala withu ntchito wakugwira makora

Vuto lomwe tili nalo ku Masasa ndi Madzi

19-Nov-2016 | 14:42

Kuno kumasasa vuto ndi madzi. madzi abwino a-Water board sanabwere komanso mjigo kulibe timatunga pa ka chitsime kosakhala bwino

Sugzo ilo tili nalo kuno ku Masasa

19-Nov-2016 | 14:32

Kuno ku Masasa suzgo ilo tili nalo ni magi. please chonde watiwvire

Njelenje atikonzere mlatho

19-Nov-2016 | 13:50

Kuno Ku Njelenje Akhasala mlatho Kulibe atiganire akamapempha ndalama ya chitukuko

Suzgo la magesi ku Masasa

18-Nov-2016 | 14:59

magetsi akusuzga kuno kumasasa

Zolozolo clinic mpaka pano *Resolved*

17-Nov-2016 | 15:36

Tati tiwakumbutse atsogoleri athu kuti Zolozolo clinic mpaka pano sitikumvako kalikonse kuti itha liti. kodi kapena ndalama sizidayende bwino

Pempho la mseu kuno ku Mtandire

16-Nov-2016 | 16:29

Kuno ku Mtandire tikupempha atsogoleri athu kuti achite chotheka atikonzere nseu. bwanji anzathu kumadera ngati ku 25 ndi ku 36 akuwapalira mseu ife ayi

Blackouts in Area 47

15-Nov-2016 | 16:32

While it is appreciated that the whole country is experiencing load shedding, the scale of load shedding in area 47 is just too much. I would urge 'equitable distribution; of load shedding with other areas.

LILONGWE WATER BOARD WATER RATIONING FROM MONDAY 14/11/16

14-Nov-2016 | 09:14

Water rationing schedule week beginning 14th November, 2016. Remember: Always use a bucket, pail, cup, NOT running water to wash clothes, utensils and brush teeth.

Kuli mapokoso kuno ku Mtandire

14-Nov-2016 | 08:34

Kuno ku Mtandire kwayamba mapokoso pankhani ya Admarc, pamalo pomwe akufuna kuyika akhansala, Azimayi amagwirapo ntchito yosamala ana amasiye. Chonde amabungwe iwafikire nkhaniyi alowererepo kuonetsetsa kuti zokhumba zandale zisasokoneze njira zina zomwe ena akuthandizikira kudera

A comment on challenges to development

13-Nov-2016 | 20:37

I would like to agree with what the councilor that was featured in the Mzinda radio program today said about the lack of a good working relationship between our leaders being a cause for lack of development in some areas. this is happening especially where the MP and Councilor belong to different parties. perhaps Councilors should not stand on a party ticket. S. Soko. Nancholi

Tiyamikire Kuyaka kwa magetsi kuno ku Likuni

13-Nov-2016 | 18:38

Kuno ku likuni tanyadila Magetsi ayaka dzulo komaso lero anangothima masana Mphatso

Tiganizireni anthu akumadera ena

12-Nov-2016 | 18:57

Ndati ndipempheko kuti ngati kuli kotheka mabungwe omwe mukupanga za Mzinda mutifikireko ife akumadera ena monga kuno ku Matawale

atikonzere ma bridge ku Masasa

11-Nov-2016 | 14:59

Kuno kumasasa suzgo ni mabridge yanyake yali kunangika