Kuno kwa Chinsapo magetsi akuvuta kwambiri. ine Kasimu wogulitsa zakumwa
Many thanks to Escom. They came through in good time after a report on Mzinda about a fault with electric lines pa Jeyi Jeyi now everything is okay and the maize mill is working. Damzy wa Swagg
kuno kwa biwi patsogolo pa 3 ways pali Gonjetso shop nseu sulibwino akonze
kuno ku mchesi m'maka kwa mfumu Pemba magetsi ayenjeza kuzima
Escom people would you pliz send men and rectify wires close to Chigayo cha Jeyi jeyi Chilinde 2 aduka. Damzy wa Swagga
Kuno ku tsabango 1 ku thanki vuto tili nalo ndi nkhani ya magetsi chonde ayesese azizima mwa size. business yanga ya chigayo idayima pano. Faison kapuchi
Kuno ku Chilomoni ward titi zikomo adazachotsa zinyala pa beehive
Sanatithandize, mpaka pano magetsi sanayakebe
Kuno Ku Nankhaka Wodi T/A Chitukula Tili Ndimavuto Awa Madzi Komanso Magetsi Koma Zonse Tinapanga Kale Apulayi Komano Magetsi Anatiuza Kut 24milion Kuchokela CP Kufikila Pa Chitukula T/C Ndikupepha Mabugwe , Aboma Ndi Ena Onse Akufuna Wabwino Kuti Atithandize Zikomo.
kuno ku Tsabango 2 kwavuta nkhani ya ma block leade. zikuoneka kuti khansala wathu ankafuna munthu wina ku Benito ndipo adawina ndiwina kotero akulephera kugwira naye ncthito. pakuchitika ziwawa
kuno ku tsabango 1 area 23 kulivuto lakuzimazima kwamagetsi chonde tikozereni pavutori
Magetsi sakuyakabe,chizimiren cha dzana kuno ku Mulunguzi,tithandizeni.
tati uthenga uwafikire bwana khansala ndi bamboo MP atikonsere nseu kuno ku Gologota Area 23 pafupi ndi nyumba ya kantwanje. Komanso ku Kaliyeka Chipasula kukafikira pa msika nsewu suli bwino. Brian Samute telela wa chinyamata
Ndati ndinenepo kuti kuno kwathu kwa Tsabango chitukuko sichikuyenda chifukwa pakuoneka kuti palibe mgwirizano pakati pa phungu ndi khansala