KUNO KU MPEMBU KULIBE MAGETSI KWAMASIKU ATATU TSOPANO.KUWAWUZA TIKUMANGOKALIPIDWA CHONDE TITHANDIZENI.KUNO KUMPEMBU KUMAKATA.
School yakwathu ilibe ma desk since 1994 anatichotsera centre yamayeso chifukwa choti palibe madesk. Mbazi L E A primary school Dedza northwest constituency.
COUNCILLOR chilomon ward mseu wa kwa nthukwa ukufunika phula
Water Rationing Schedule for week beginning Monday 24th October to Sunday 30th October, 2016. Remember although we are doing all the best to save the little water that we have, LWB reservoirs (Kamuzu Dam I and II) are fast being depleted. Always use a bucket, pail, cup, NOT running water to wash clothes, utensils and brush teeth.
Kuno ku Dedza North west constituency-Magomero . MP wathu Alekeni Menyani uthenga uwu umufike: Nseu kuchoka pa ndyampho bridge kukafika pa Lobi suli bwino komanso pa Mbazi school abweretse ma desk. ine Simon Jovinal carpenter
kuno ku msika wa ndirande zinyalala ziri pali ponse.Akhonsolo achitepo kanthu.
Ndati ndikambepo kuti tidapempha kudzera mwa atsogoleri athu pa kanthawi ndipo tidakali kudikilira kuti achitepo kanthu pa mavuto omwe ali pa sukulu ya Makata primary. ma toilet ogwira ntchito alipo atatu okha koma pali ma sauzande chiwerengero cha ana omwenso aziphunzitsi awo ndi ochepa. ine Kenson Malango kwa Chinseu.
Pali vuto kuno kundilande'pa brige yapazambiya padzadza zinyalara-chonde tinthandinzeni.
kuno ku Kawale 1 nseu wa ku Block A kuchoka pa Banja la mtsogolo sulibwino . ukakhala chomwechi ikabwera mvula pavuta
School yakwathu ilibe ma desk since 1994 anatichotsera centre yamayeso chifukwa choti palibe madesk.
kuno kwa senti kwa chimoka tufuna mjigo. Ine mayi mnjedza wa thobwa
Remember LWB reservoirs (Kamuzu Dam I and II) are fast being depleted. Always use a bucket, pail, cup, not running water to wash clothes, utensils, brush teeth. SMS LWB to 253 for updates on the water situation.
ndati ndiyamike kuti khansala wathu wa Nyama ward ntchito akuigwira. Chilimbikitso chawo pa Community police chakhwimitsa chitetezo kuno
Area 24 mavuto ndi ambiri tiuzileni a MP zamavuto aza madzi, miseu mijigo ndinso ESCOM nkhani ya magetsi. t
I have to say there has been a slight improvement in power supply over the last week here in Area 25... we've had power for longer hours than before, I hope we maintain this trend