Tukhumba mseu watala kuno ku Hilltop

20-Nov-2016 | 16:58

Kuno ku masasa mpaka hilltop tar kulibe koma kukumangidwa nyumba zabwino

Atithandize ndi mlatho kuno ku Solzbery lines

20-Nov-2016 | 14:57

Tati tipempheko kuti atithandize ndi mlatho kuno ku Solzbery lines mzuzu

Yankho pa pempho la mseu ku Zolozolo

20-Nov-2016 | 13:48

mukunena miseu yonse kapena umodzi? ndipo para niumodzi uli mwa blockleader njani? Stafford Khunga - Khansala

Atikonzere nseu kuno ku ZoloZolo

20-Nov-2016 | 04:45

Tati tipemphe nawo kuti Khansala wathu kuno ku Zolozolo east atikonzere nseu wa kwa BagiDadi

Ku Masasa bridge ayikonze mvula isanafike *RESOLVED*

19-Nov-2016 | 21:04

Ku masasa bridge ya chideso ndiyoonongeka moti mvula ikangogwa sizikhala bwino. Martin wallace

Mseu wa ku Luwinga turnoff ya ku Paramount sulibwino

19-Nov-2016 | 21:02

Kuno ku Luwinga mseu wa pa turnoff ya pa Paramount Lodge sulibwino ukufinika maintenance. Ndine Edith Mhango

Suzgo la maji ku Chasefu

19-Nov-2016 | 15:40

Kuno ku Chasefu suzgo ni maji kulekaleka

Tiyamike kuno ku Likuni

19-Nov-2016 | 15:15

Kuno ku likuni ndakunyadilani Magetsi ayaka dzulo komaso lero anangothima masana Mphatso

Magesi akuzimazima kuno ku Mchengautuwa

19-Nov-2016 | 15:03

Ife kuno ku mchengautuwa vuto ndila magesi kuzimazima

Njerenjere road needs maintenance

19-Nov-2016 | 15:02

Kuno ku mchenga utuwa njerenjere road need maintenance

Hilltop atikonzere mseu

19-Nov-2016 | 15:02

Ku hilltop msewu ukusugza nyengo ya mvula

Pempho kuno ku Mchengautuba *Resolved*

19-Nov-2016 | 15:01

Ku Mchenga Utuwa Atithandizeko Mwachangu kukonza mseu. Prince Chavinda

Zolozolo magetsi akuvuta kwambiri

19-Nov-2016 | 15:01

Kuno ku zolozolo magesi yakusuzga tikugona mumudima

Ukhondo sulibwino ku Masasa

19-Nov-2016 | 14:59

kuno ku masasa ma barber man yotaya sisi bweka am vincent doesmatter

Vuto la magesi ku Geisha Mzuzu

19-Nov-2016 | 14:59

kwanthu ku gesha vuto ndi magetsi ndine tionge

Zolozolo suzgo la Mseu

19-Nov-2016 | 14:58

Kuno ku Zolozolo suzgo likulu ndi Mseu uli makora yaye