KUNO KUMULANJE LIMBULI KULI MAVUTO AAKULU KUMBALI YA AKHANSALA ADASEGULILA NSIKA WA LIMBULI KOMA KUMANGA NSIKAWO SIKUNATHE
mutiunikilepo kuti kasi ntchakwenerera kuwezga mwana wa school kuti wakatole ndalama ya chitukuko , mayeso apo wanyake wakulemba mayeso? Kuno ku zolozolo tiphulani mu suzgo ili of which tindafike pa conclusion kuti tipereke ma 3000 poti apo wakachemeska tawapapi tikakana amount iyi kweni wasambizi wawezga wana cos of this money of which boma likukana kuti primary level njaulele except ndalama yamayeso
Water Rationing Schedule for week beginning Monday 28th November, 2016 to Sunday 4th November, 2016. Yes the rains have started but it is still important to use water wisely. Remember to use water just enough for your needs. Always use a bucket, pail, cup, NOT running water to wash clothes, utensils and brush teeth. If you have problems with these messages please do not hesitate to contact the Public Relations Officer BRIGHT SONANI. Thanks
akhansala kapena MP adera lathu, tithandizeni(ife Aphunzitsi ndi ophunzira pa Lizulu Primary school) potikozera Mzamani ground.Mr M.I Shaba.Lizulu,Ntcheu.
kuno ku Nsanje mvula yayambapo ndye ndi mango zati mbwee zofunika azaumoyo achite watchout
Kuno ku Dwangwa ukasi area za mumtoilet zimacita kuyenda ngati mtsinje m'manyumba mwathu. akhonsolo achitepo kanthu
Magetsi-kuno ku Chilomoni Mulunguzi magetsi chizimireni cha dzana masana friday pa 25 mpaka lero osayaka,zikukhala bwanj? Poti madera anzathu onse akuyaka.
KUNO KUMULANJE LIMBULI KULI MAVUTO AAKULU KUMBALI YA AKHANSALA ADASEGULILA NSIKA WA LIMBULI KOMA KUMANGA NSIKAWO SIKUNATHE
ESCOM should please if possible work on solving this regular power outage problem once and for all. here in Zomba St. Marys to be exact we have had no electricity since yesterday evening, this is beyond load shedding
I would like to report that we have had no water here in Nancholi around the market since yesterday morning.
Ndikupempha ngati kuli kotheka pa mjirijiri butchery tikamapita pa 4ways ya king shaka bar bridge linabooka komanso tikamapita ku ching'ambo from up chiputula primary pafupi ndi seventhday church. andrew chavula concerned citizen
Water Rationing Schedule for Week beginning Monday 21st November 2016. We really appreciate for your support and understanding.
area 23 tsabango 2 mseu wadon bosco please tikozereni akhasala
Kuno ku Bangwe tikuthokoza adatikonzera nseu wochoka mthandiza kudutsa pa chinjinga kupita ku clinic kodi nanga wa ku Namatapa bwanji..?
Kuno ku Chibanja ward tikufuna ma dreni m'bali mwa mseu kupangira nthawi ya mvula