Yankho pa kusaoledwa kwa Zinyalala pa Nsika wa Mtandile

29-Aug-2016 | 19:59

Chigalimoto sichifikadi kuzaola zinyalala chifukwa nsika wa Mtandire amapanga collection ya ma market fees okha.Pano pali kukambirana kuti City Council izitolela yokha ma fees pambuyo pake chigalimoto chizibwera. A Soko. Cllr Mtandile Ward

Dealing with leakages around your home/premises

29-Aug-2016 | 11:55

Without much information it indeed sounds not possible to deal with leakages around the home. But here is how. And the good thing is you are not only saving water but you are also saving yourself from paying huge water bills.

Tiyamikire Atsogoleri Athu

29-Aug-2016 | 08:48

Ndati ndiyamike atsogoleri athu kuno ku Area 25 Kabwabwa ward pokonza dongosolo lopala nseu wopita ku Chiuzimba

Lilongwe Water Board Rationing Schedule beginning 29/08/16

26-Aug-2016 | 14:16

Water Rationing Schedule from Monday 29th August to Sunday 4th September, 2016. Remember to use water wisely. SAVE WATER, SAVE YOUR CITY OF LILONGWE. Avoid using hose pipes when washing vehicles, watering your grass and flower lawns or gardens. Please ensure that your home is free of leakages and close all taps tightly after use.

Improvement in Water Supply

23-Aug-2016 | 17:41

I would like to thank the Lilongwe water board for improving the water situation in area 49. if am not wrong it has now been two weeks with continued supply of water, please continue.

Kodi tingadziwe bwanji zakuzima kwa magesi?

23-Aug-2016 | 11:32

Ndati ndifunseko nawo kuti kodi tingathe kudziwa bwanji kuti magetsi azima komanso kuyaka nyengo yanji?

Waste Collection

23-Aug-2016 | 09:52

Zinandisangalatsa kuwona a city akudzatenga zinyalala mudela lathu izi ndi zithu zabwino ndipo mupitilize a city koma pa msika wa old gualiver pali zinyalala ndipo sipawoneka bwino komaso pamanunkha chonde mudzatiwoneleko kuno ku gualiver, area 49.

Lilongwe Water Board Rationing Schedule

23-Aug-2016 | 07:05

Water Rationing Schedule from Monday 22nd August to Sunday 28th August, 2016. Please remember to use water wisely by avoiding using hose pipes when washing vehicles, watering your grass and flower lawns or gardens. Please ensure that your home is free of leakages and close all taps tightly after use.

Khansala wa dera langa sindimudziwa

22-Aug-2016 | 20:52

Khansala wa dera limene ndikukhala sindikumudziwa thandizeni. kwa Phwetekere

Atikonzere Nseu wa Salima

22-Aug-2016 | 20:40

Kuno ku salima msewu wathu sulibwino,okumbika komaso ndiwaung'ono kuchokera ku salima depot kupita ku sengabay Livingstonia,road signs ulibe koma ndiomwe umakhala busy nthawi zonse.tithandizeni pliz.Ine Richard katengeza,ngolowindo village,TA maganga

Kuthokoza Khansala Pokonza Mseu

22-Aug-2016 | 08:31

kuno ku ntandile tithokoze khansala poika ma ring mu nseu

Yankho pa pempho la Mjigo ku Area 24

22-Aug-2016 | 00:01

Nkhani ya mjigo ndikuidziwa ndipo ndinapempha kuti choyamba amfumu akhazikisepo komiti yoyang'anira mjigowu. Ndipo ndalama zokhonzera ndipereke kwa komitiyo osati kwa munthu m'modzi. E. Botha. Councilor Ngwenya Ward

Kuvuta kwa Madzi kwa Chinsapo

21-Aug-2016 | 16:23

Kuno Kwa Chinsapo Madzi Akuvuta Mutithandize Mai Mwanya

Area 23 Nseu wopita ku Don Bosco

21-Aug-2016 | 16:20

Kuno ku Area 23 bwana MP ationereko nseu wopita ku Don Bosco.. tikuthokoza adathira miyara malo ena koma ena sadathire. tikuopa kuti nthawi ya mvula ikafika nseu uzavuta

Tiyamikire Mzinda

21-Aug-2016 | 15:13

zikomo kwambiri a-Mzinda chifukwa chopereka mwayi woti titha kumalemba ma uthenga pa mavuto akudera

Pempho Kwa Anzanga Kuno Kwa Senti

21-Aug-2016 | 13:39

Kuno kwa Centi zinyalala timangotaya paliponse, penpho langa nali, tiyesese pa tokha ngati anthu amudera kutaya zinyalala mosamala