Uthenga ufikileko ESCOM, magetsi Akungozimazima. Ndine Charity Kuchokera Ku Area 25 Sector 7
Kuno ku Area 25 magetsi akuzimazima mutithandize. Mayi Chanache
Kuno kwa Chilinde tikuthokoza chifukwa chotikonzera nseu wochoka pa Parish, achite chimodzi modzi ndi miseu yina yofunika kupala
Kuno kwa MtsiliLza kuli vuto lakuzimazima kwamagetsi ndine harry chalanda
Likuni we are having problems of Electricity, as much as we understand the Load shedding program koma kuno kuthima thima kwayenjeza
kuno kwa cent kumsika kulibe bin yotailamo zinyalala moti anthu amangotaila pena paliponse zinyalala. Atipatse Bin
kuno kwa Senti pali vuto lokonza mseu, pakuoneka kuti pali kukokana nde zaima
Kuno ku Mchesi ngati kuli kotheka chi galimoto chotenga zinyalala chizidutsa kawiri. kanthawi komwe sichikudutsa ukhondo siukutheka
Magetsi akuvuta angozimazima kuno ku area 49 Gulliver
kuno kwa senti magesi ndi vuto, aunike bwino ma line podula-nkuyatsa tumakhala nyengo yaitali mu mdima
Magesi ndi madzi akumavuta kuno ku Area 18
Kuno ku Chilinde 1 madzi akuvuta kwambiri. Azimayi tikuvutika
Kuno ku Kawale 1 atikumbire mjigo kuti tizithandizikapo malingana nkuvuta kwa madzi
Our MP should lobby for the support of MRCS to construct toilets at Kaufulu primary as they have done in other primary schools through their WASH project. I feel sorry when am passing through the school and see the toilets that they use. It has to be understood that a good learning environment is essential
Bwana MP atithandize kuno ku Chimwankhunda nseu wopita ku chihema nkale adalonjeza atikonzere