Sabata imeneyi magetsi ayaka bwino kuno ku Bangwe

25-Jan-2017 | 12:15

kuno ku Bangwe vuto linali kuthima kwa magesi koma sabata yathayi zinali bwino

Magetsi akuvuta ku Tondole

23-Jan-2017 | 08:33

Kuno ku Namiyango area ya cha pa Tondole magesi akumavuta kwambiri

Magetsi akuvutabe kuno ku Ndirande

22-Jan-2017 | 02:47

Magetsi akumazimazima kuno ku Ndirande.

Kuno ku Ndirande Vuto ndi Magetsi

27-Jan-2017 | 02:47

Magesi akuvuta kuno ku ndirande.

Vuto lakuzimazima kwa magetsi likupitirira kuno ku Ndirande

16-Jan-2017 | 10:47

Tati tidandaule nkupanga report kuti kuno ku Ndirande vuto lakuzimazima kwa magetsi likupitirira. chonde atithandize.

Problems that we experience in Chilomoni

26-Jan-2017 | 07:41

I would like to report that the main problems that we experience here in Chilomoni are water and electricity. service delivery in these two ares is not so good

Magetsi akuvuta kwambiri kuno ku Mbayani

28-Jan-2017 | 04:07

Magesi akuvuta kwambiri kuno ku Mbayani. Ndine ulemu majiga

Vutu lakuzima kwa magetsi

28-Jan-2017 | 07:28

Kuno ku Zomba kwa Mpondabwino tili ndi vuto lakuzimazima kwa magetsi. Ine Lemusi Kawanga

Power is a persistent problem here in Machinjiri

30-Jan-2017 | 03:19

My name is Peter Kamama,from Khama Machinjiri, I would like to report that our biggest problem is power. We usually have supply only thrice a week.

Tiyamikire kuyaka kwa magetsi kuno ku Chikwawa

31-Jan-2017 | 03:26

Ife Kuno Kuchikwawa T/A Chapananga V/G Lackson Mudera Mwathu Magetsi Alipo ndipo amayaka bwino Ine F.Stephano.

Improvement in Power Supply

01-Feb-2017 | 08:42

I would like to commend ESCOM for the improvement in power supply here in Area 23. Great work team ESCOM.

Tiyamikire ESCOM pa kayakidwe ka magetsi

06-Feb-2017 | 08:41

Ine ndi Irvin Chadeka kuno ku Area 25 sector 7, ndati ndiyamikire ESCOM chifukwa cha kayakidwe ka magetsi kuchokera mid January kufikira pano magetsi akuyaka bwino kulekana ndi kale pomwe amazimazima.