AREA 25 Magetsi akuzimazima

19-Aug-2016 | 10:05

Kuno ku Area 25 magetsi akuzimazima mutithandize. Mayi Chanache

Kuzimazima kwa Magetsi Area 25 Sector 7

19-Aug-2016 | 10:11

Uthenga ufikileko ESCOM, magetsi Akungozimazima. Ndine Charity Kuchokera Ku Area 25 Sector 7

Kuzimazima kwa Magetsi kwa Mtsiliza

12-Aug-2016 | 13:42

Kuno kwatsiliza kulivuto lakuzimazima kwa magetsi ndine harry chalanda

kuzimazima kwa magetsi kwa Mtsiliza

19-Aug-2016 | 01:37

Kuno kwa MtsiliLza kuli vuto lakuzimazima kwamagetsi ndine harry chalanda

Magetsi achepetse kuzima nthawi yaitali

02-Sep-2016 | 05:40

magets akuyenera kumayaka nthawi yayitali kumazima nthawi yayifupi mwandimva kuno ku 25

Nthawi Ya kuzima kwa Magetsi

08-Sep-2016 | 08:55

Kuno ku area24 magetsi ndi chifukwa chani amazima mammawa kwambiri anthu tikukonzeka za kutchito ndi ku school

No Power Outage in Chilinde

09-Sep-2016 | 13:30

I would like to commend ESCOM for the consistent supply of power in Chilinde newlines. Ever since I moved in about a month ago magetsi sanazimeko. I can only hope the same would be realized ku madera ena.

Taonako kusintha nkhani ya magetsi

20-Sep-2016 | 05:56

magetsi akuyaka moyenera kuno ku Dzenza sakudandaulitsa kwenikweni akuyesesa nsanamepo apa.

Kuzima kwa magetsi ku Chilomoni - Mulunguzi

04-Oct-2016 | 16:42

kuno ku Chilomoni Mulunguzi,magetsi azima dzulo pa 3 October m'mawa mpaka pano lero sakuyaka,tithandizeni

Kuzimazima kwa Magetsi ku Chitedze

04-Oct-2016 | 08:33

Magetsi kuno ku Chitedze-Lilongwe awonjeza kuzima

Persistent Blackouts

05-Oct-2016 | 08:27

In as much as we understand the challenges our service providers may be facing but with regards electricity I would say we have reached our lowest point as a country. in Area 25 we are at times only having power for 5 hours in a day and at night for that matter when we have to rest and be sleeping. Please ESCOM assist us, last time I heard about the possibility of tapping power from Mozambique where are we with this.

Kuzima kwa magetsi kwafika pena

05-Oct-2016 | 12:40

Kuno ku Area 49 nkhani ya kuzima kwa magetis yafika pena, amayaka usiku 10 koloko nkuzimasa m'mawa 5 koloko. nde pamenepa amati ife tigwritse ntchito magetsi nthawi yanji ?