Street Lights Not Working *Resolved*

13-Jul-2018 | 18:50

Some street lights along Tsirinana road in Limbe are not working. Please assist

Pempho loti atikonzere Msika ndi Sukulu

25-Jul-2018 | 14:14

Ku Chilomoni kwa Nthukwa pempho ndi loti atikonzere msika amalonda tachuluka malo akuchepa. Komanso Sukulu ana akuchulukamo aphunzitsi kuchepa ndi malo okhala

Nsika wa Limbuli udayima

01-Dec-2016 | 15:50

KUNO KUMULANJE LIMBULI KULI MAVUTO AAKULU KUMBALI YA AKHANSALA ADASEGULILA NSIKA WA LIMBULI KOMA KUMANGA NSIKAWO SIKUNATHE

Consideration To Vote Where We Registered

20-May-2019 | 02:46

We try to build a better Malawi by choosing proper leaders and it is very disheartening to note tht only journalists wl b allowed to vote at any polling station and not the versity students who r away from there homes where they registered. Plz if possible fight for us. Tivotele kuma polling center akufupi nd school, lets vote for our better Malawi. Polytechnic

Campaigning Outside Campaign Period

19-May-2019 | 14:51

A vehicle branded with party colours, Toyota NOAH reg no BU7810 is still campaigning. Giving out phones and party clothes to people.

Tachedwerako Kuyamba Kuvota Kuno

21-May-2019 | 06:12

Nampati Polling Station kuno Thyolo anthu ayamba 6:06am kuvota timayembekeza kuti atsegula ikamati 6:00am