Tiwonge kuno ku Jombo ward

19-Nov-2016 | 14:56

Jombo ward Khansala withu ntchito wakugwira makora

Nsika wa Limbuli udayima

25-Nov-2016 | 16:58

KUNO KUMULANJE LIMBULI KULI MAVUTO AAKULU KUMBALI YA AKHANSALA ADASEGULILA NSIKA WA LIMBULI KOMA KUMANGA NSIKAWO SIKUNATHE

Chitukuko ndi chotheka ngati pali kugwirirzana

04-Dec-2016 | 15:49

Ine filimon kuno kuchikuli. ndati tinenepo kuti MP akuyenela kugwilizana ndi khasala wake chitukuko chitheke

Chitukuko chikukanika chifukwa cha kusagwirizana

27-Oct-2016 | 10:17

Ndati ndinenepo kuti kuno kwathu kwa Tsabango chitukuko sichikuyenda chifukwa pakuoneka kuti palibe mgwirizano pakati pa phungu ndi khansala

A comment on challenges to development

13-Nov-2016 | 20:37

I would like to agree with what the councilor that was featured in the Mzinda radio program today said about the lack of a good working relationship between our leaders being a cause for lack of development in some areas. this is happening especially where the MP and Councilor belong to different parties. perhaps Councilors should not stand on a party ticket. S. Soko. Nancholi

Ndemanga pa nkhani ya achinyamata

18-Dec-2016 | 18:59

ndati ndithirepo ndemanga pa nkhani ya achinyamata yomwe mumakambirana mu puloglamu ya pa radio lero. Palibe munthu wachikulire amene angakane kugwira ntchito ndi achinyamata, pokhapokha ngati pali chokaikitsa pa machitidwe ndi khalidwe la anyamatawo. Achinyamata tili nawo m'makwalalamu, kuchulukana ULESI. Ambiri akangophunzira pang'ono angofuna kufikira pa mpando olamulira, oyang'anira osafuna kugwira dotting. Kudzitukumula pakati pa akulu. Iai, dziwani kuti ngakhale adindo, atsogoleri a lerowa sanangofikira pamenepo. Nawonso Analinso achinyamata. Tatiyeni tidekhe, tiphunzire kuti tidzakhale adindo odalilika. You want to come from the classroom, straight into the State House! No, let us have time to learn the works in order to gain experience. I am Gogo Phiri in A49.

Tikusowa chithandizo kuno kwa Mtsiliza

18-Dec-2016 | 16:01

Kuno ku lilongwe city west timangomva mmadera azathu chitukuko kunoko kwa mtsiliza ndimavuto chonde tingapite kuti kuti adundo athu atifike moti sitiwadziwa. Ine okhudzidwa ndi dera langa Harold phili

The youth and development

18-Dec-2016 | 17:04

I am Victor Dzimbiri from Kawale 2. I would like to comment on today's Mzinda radio program about the participation of the youth in development. I wish to say that here in Kawale there is a youth centre near Masintha hall but there is no initiative from our leaders or organisations to make it work. if they can take the initiative to involve us we are ready to utilise it

Some street lights not working *Resolved*

07-Oct-2016 | 08:41

some street lights along the road from kanengo 3 ways to area 25 are not working

Tikuthokoza kuno ku Ndirande

27-Dec-2016 | 18:33

m'mene unangopangika msonkhano kuno ku Ndilande wozamisa demokalase kudela lathu pano anthu otolela ndalama pa mwamba pa yomwe timapereka kale ya market fees anasiya.tikukhulupirira kuti izi ndi chifukwa cha msonkhano wa tilitonse pomwe tidapasidwa mwayi wofunsa aChairman amu nsika ndi a-Khonsolo ya mzinda wa Blantyre kuti afotokoze bwino kuti ndalama imeneyi imapita kuti chifukwa chitukuko sitimachiona.

Elections of Mayors

06-Jan-2017 | 05:27

I would like to congratulate our friends in Lilongwe City for the election of a new mayor and would like to say we hope for the same here in Mzuzu. As for us citizens it is high time we really were vigilant to question the execution of duties by Mayors, our leaders make promises time and again but because we do not strive to engage with them and check progress our cities are not developing. Malange, Luwinga.

Tikupempha chithandizo kuno ku Chiradzulu

05-Jan-2017 | 17:36

Ife kuno ku chiladzulu zatibvuta kumbali yafeteleza,pempho lathu kuno mutatifusila unduna wa wazamalimidwe kuti ife anthu akuchiladzulu feteleza kulibe tizikagula kuti makamaka kuchiladzulu south,chimanga pano chikumasula tithandizeni, ndimakoponiwa makampani wobweletsa feteleza kuno sakubwela anthu akubvutika kwambili,ndiye programe ya m'zinda imatithandiza. Ine odandaula Evasi Wasi Mpethela