Zili sharp. very welcome. its good kuti tikhala nako kuthekera kutsata kuti makhonsolo athu ndalama zikuyenda bwanji. Tikhala tikufuna kudziwa nawo mmaka ndalama zopita ku maphunziro. masukulu akuchepa. Haji Shumba Zomba
I would like to express my appreciation to Lilongwe city council for works on the road at the turn in Forz from Malangalanga. We had complained for so long
area 23 tsabango 2 mseu wadon bosco please tikozereni akhasala. Komanso escom ndi water board akuyenjeza
ESCOM is planning to undertake major upgrade works that will affect the Central and Northern regions as per the attached notification.
Ndati ndipemphe aku Escom kuti abwere adzationere nthambo za magetsi kuno ku Sigerege Chilomoni. Pamene nthambo zikuchoka pa polo kubwera pa nyumba yathu pakufuka utsi kotera pano ma switch tangogwetsa kupewa ngozi, Kuchoka pa Rayelo nseu woyamba kumanja pa kona ya AMasamba. Ine Mai chisale
Kuno kwathu kwa kanthonga, Nankhaka ward khalidwe la akuba likunka nichuluka, mwina chifukwa police nku Lumbadzi ndi Kanengo nde anthu amasibwa kuona kuti nkutali. Atsogoleri athu atithandize
Pa Makhetha clinic tati tipemphe nawo kuti atikonzere ma Toilet, anadilizika
Ku Chilomoni kwa Nthukwa pempho ndi loti atikonzere msika amalonda tachuluka malo akuchepa. Komanso Sukulu ana akuchulukamo aphunzitsi kuchepa ndi malo okhala
Yesterday was worse we did not have electricity not even for some minutes its getting worse please please help us......here in Likuni
Kuno kwa chinkhwiri kwa T/A Chakhaza ESCOM inazayika kalekale ma polo amagetsi ndipo anthu anawapangitsa wiring manyumba mwawo za changu changu koma its now a year transformer siinabwere,,,,,pliz help us
Some street lights along Tsirinana road in Limbe are not working. Please assist
I would like to express my concern with ESCOM on the regular cutting of power in our area around Likuni. It is very disheartening.
Chinsapo pempho nali. Atikonzere nseu wopita ku Kakule primary school
Tati tipempheko kuti atithandize ndi mlatho kuno ku Solzbery lines mzuzu. Komaso tikapita ku health center amachedwa kutithandiza
There is a burst water pipe in Chinyonga, on the turn to Bedir schools house number 2