On behalf of the people from Dowa, Bowe area to be specific I would like to send out a request for a new police unit for the area. The current station as you can see in the attached picture is terrible.
Kuno ku Katawa kuli suzgo lakuti para wanthu wakoleka kuti wali kwiba vinthu nakuluta kupolice wakuchedwa yayi kufuma. So para ivi vikuchitika tingalutaso nkhu.? ka uko tikumanya kuluta na ma suzgo aya ni ku police
Kuno ku Mchengautuba west unkhungu ngunandi. Community police yuchitapo kanthu yayi
Mchengautuba west akuba akuvuta kwambiri m'maka kwa Belewa sitikudziwa kuti atsogoleri athu malingaliro awo pa nkhani imeneyi ndi otani
Kuno kwathu kwa kanthonga, Nankhaka ward khalidwe la akuba likunka nichuluka, mwina chifukwa police nku Lumbadzi ndi Kanengo nde anthu amasibwa kuona kuti nkutali. Atsogoleri athu atithandize
Ine ndati ndipempheko ku khonsolo kuti itikonzere ti migula kapena kuti ngalande zodutsamo madzi pa msika wa Malingunde. Atatikonderanso nkumanga ma shade zingakhale bwino mmaka chitetezo cha pa msika
Katawa kuba kwachuluka police sikutithandiza. Komanso magetsi
We people of Nsundwe are living in fear because the police are not available since that incidence of Police raping our women and girls
Kuno ku Kasungu Chitetezo chachepa anthu akumalanga okha akuba. chonde tithandizeni
Balaka Shire ward umbava wavuta ku Mwima. Every week kumapezeka shop yabedwa