Lwezga health centre opening OPD only half days from Mondays to Fridays
Hello, wanted to report on poor waste disposal of chibanja people opposite the Airport and Matabwa mkt
Chibavi east tili ndi vuto la chipatala,anamanga clinic in 2006 koma mpaka pano ndi under five clinic basi,koma timafuna ikanakhala full clinic ndipo itha kuthandiza anthu aku Chibavi west,Mchengautuwa East and West,and chibanja. Well wisher watimangila mpanda 2month ago
Chipatala cha Mwima chatha zaka 17 koma osachitsegulila. Anthu adandaula koma kuli zii
Ndati ndipemphe nawo chithandizo choti khonsolo itibweresere bin yayikulu pa msika wa Apostolic. Malowa akubweresa chiophyezo cha matenda chifukwa anthu zinyalala akungotaya mosasamala
Ine pempho langa likunka kwa khonsolo la Mzinda wa Blantyre. Aunikepo zakuvomereza malo kupangirapo bizinesi. Nkhani yanga yagona pa Rest House yomwe yamangidwa pafupi ndi Mpingwe Primary school, makolo akudandaula kuti ikulimbikitsa khalidwe loyipa mwa ana