Verified

  • 17-Aug-2017 | 07:12

Azachose Zinyalala Pa Msika Wa Mbayani *Resolved*

Kuno ku Mbayani pa Msika inde tikuyamika kuti anatipasa bin koma akumazengereza kuzachosa bin ikadzadza. Ngati pano sabata yonseyi sanabwere. Chonde atithandize.

Location