Verified

  • 07-Feb-2017 | 00:32

Mgwirizano Ku Nankhaka Ward - Lilongwe

Kuno ku Nankhaka ward mu mzinda wa Lilongwe ndati ndiyamikire za mgwirizano omwe anthu ali nawo pa nkhani za chitukuko. titabwera pamodzi kugwira ntchito yokumba dam ya nsomba pano anthu anabweranso pamodzi kulima mbewu. Zonsezi ngati njira yowonetsetsa kuti patakhala kusowa kwa chakudya pakati pa anzathu ena ku ward, tithe kuzithandiza mwa ife tokha. Cllr W Kapiza

Location